Mondadori Store

Trova Mondadori Store

Benvenuto
Accedi o registrati

lista preferiti

Per utilizzare la funzione prodotti desiderati devi accedere o registrarti

Vai al carrello
 prodotti nel carrello

Totale  articoli

0,00 € IVA Inclusa

"Tuluka, nupite kumiseu ndi njira za kuminda, nuwaumirize anthu alowe. KUTI NYUMBA YANGA IDZALE." Luka 14:23. Kulira kwa Mulungu ndi kwakuti dziko lonse lipulumutsidwe, ndi kuti nyumba Yake-tchalitchi-lidzale!
Kuchokera ku vumbulutso limeneri bukhu iri linabwera., "Mpingo Waukulu" lolembedwa ndi Bishop Dag Heward-Mills, m'busa wa umodzi mwa mipingo yaikulu kwambiri ku Ghana. Mpingo wanu ndi utumiki wanu sudzakhalanso chimodzi modzi mukawerenga bukhu lolimbikitsali!"Dr. Heward-Mills ndi wodzipereka kwa Ambuye Yesu Khristu ndi ntchito yotenga mbali pa kulalikira ku dziko lonse. Ndi mtsogoleri wamphamvu ndinso chitsanzo ku mautumiki onse, ndipo ife ku "Church Growth International", ndife olemekezedwa kudziwa ndikumutcha Dr. Dag Heward-Mills mnzathu komanso wogwira naye limodzi ntchito mu kholola lalikulu mu minda ya padziko."
-Dr. Yonggi Cho
Wamkulu, Church Growth International

Dettagli down

Generi Religioni e Spiritualità » Cristianesimo

Editore Dag Heward-mills

Formato Ebook (senza DRM)

Pubblicato 13/06/2019

Lingua

EAN-13 9781643292335

0 recensioni dei lettori  media voto 0  su  5

Scrivi una recensione per "Mpingo Waukulu"

Mpingo Waukulu
 

Accedi o Registrati  per aggiungere una recensione

usa questo box per dare una valutazione all'articolo: leggi le linee guida
torna su Torna in cima